komadi ndi zowona..hey how you doing .....me just trying to keep with life mate.komande umakumbukira bwanji ...koma utandiuza your real name ndithakukudziwa ....by the way are you now ?
take care..
At 10:07am on September 3, 2008, Eunice Mtali said…
Aaah inenso sindinapange connect kuti ndi kenakake ka chipani. Koma siyanga tshirt imeneyo, ndi ya aneba - umadziwa, living in a community kumayanika zovala limodzi. All good.